Psalms 12:2 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Aliyense amangonamiza mnzake, amathyasika ndi pakamwa pake, amalankhula ndi mitima iŵiri.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Amanena za bodza munthu yense ndi mnansi wake, amanena ndi mlomo wothyasika, ndi mitima iwiri.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Aliyense amanamiza mʼbale wake; ndi pakamwa pawo pabodza amayankhula zachinyengo.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Amanena za bodza munthu yense ndi mnansi wace: Amanena ndi mlomo wotyasika, ndi mitima iwiri.