Psalms 12:4 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Paja anthu amenewo amanena kuti, “Tidzapambana ndi mau athu, pakamwa tili napo, nanga angatigonjetse ndani?”
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
amene amati, Ndi lilime lathu tidzaposa; milomo yathu nja ife eni; mbuye wa pa ife ndani?
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Pakamwa pamene pamati, “Ife tidzapambana ndi kuyankhula kwathu; pakamwapa ndi pathupathu, tsono mbuye wathu ndani?”
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Amene amati, Ndi lilime lathu tidzaposa; Milomo yathu nja ife eni; mbuye wa pa ife ndani?