Psalms 12:6 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Malonjezo a Chauta ndi angwiro, ali ngati siliva womkometsa m'ng'anjo yamoto, woyeretsedwa kasanunkaŵiri.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Mau a Yehova ndi mau oona; ngati siliva woyenga m'ng'anjo yadothi, yoiyeretsa kasanu ndi kawiri.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Ndipo mawu a Yehova ndi angwiro monga siliva oyengedwa mʼngʼanjo yadothi, oyengedwa kasanu nʼkawiri.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Mau a Yehova ndi mau oona; Ngati siliva woyenga m'ng'anjo yadothi, Yoiyeretsa kasanu ndi kawiri.