Psalms 120:2 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Ndimati, “Pulumutseni, Inu Chauta, kwa anthu onama ndi kwa anthu onyenga.”
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Yehova, landitsani moyo wanga kumilomo ya mabodza, ndi kulilime lonyenga.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Pulumutseni Yehova ku milomo yabodza, ndi kwa anthu achinyengo.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Yehova, landitsani moyo wanga ku milomo ya mabodza, Ndi ku lilime lonyenga.