Psalms 120:4 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Adzakuzunzani ndi mivi yakuthwa ya munthu wankhondo, pamodzi ndi makala amoto a mtengo wa tsanya.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Mivi yakuthwa ya chiphona, ndi makala tsanya.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Adzakulangani ndi mivi yakuthwa ya munthu wankhondo, ndi makala oyaka a mtengo wa tsanya.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Mibvi yakuthwa ya ciphona. Ndi makara tsanya.