Psalms 120:5 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Ndili ndi tsoka lalikulu, chifukwa ndimakhala pakati pa anthu onga mbuli za ku Meseki ndi Kedara.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Tsoka ine, kuti ndili mlendo m'Meseki, kuti ndigonera m'mahema a Kedara!
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Tsoka ine kuti ndimakhala ku Mesaki, kuti ndimakhala pakati pa matenti a ku Kedara!
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Tsoka ine, kuti ndiri mlendo m'Meseke, Kuti ndigonera m'mahema a Kedara!