Psalms 120:6 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Ndakhala nthaŵi yaitali pakati pa anthu odana ndi mtendere.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Moyo wanga unakhalitsa nthawi pamodzi ndi iye wakudana nao mtendere.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Kwa nthawi yayitali ndakhala pakati pa iwo amene amadana ndi mtendere.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Moyo wanga unakhalitsa nthawi Pamodzi ndi iye wakudana nao mtendere.