Psalms 121:1 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Ndimakweza maso anga ku mapiri. Kodi chithandizo changa chimachokera kuti?
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Nyimbo yokwerera. Ndikweza maso anga kumapiri: Thandizo langa lidzera kuti?
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Nyimbo yoyimba pokwera ku Yerusalemu. Ndikweza maso anga ku mapiri; kodi thandizo langa limachokera kuti?
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndikweza maso anga kumapiri: Thandizo langa lidzera kuti?