Psalms 121:2 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Chithandizo changa nchochokera kwa Chauta, amene adalenga kumwamba ndi dziko lapansi.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Thandizo langa lidzera kwa Yehova, wakulenga zakumwamba ndi dziko lapansi.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Thandizo langa limachokera kwa Yehova, wolenga kumwamba ndi dziko lapansi.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Thandizo langa lidzera kwa Yehova, Wakulenga zakumwamba ndi dziko lapansi.