Psalms 121:6 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Dzuŵa silidzakupweteka masana, mwezi sudzakuvuta usiku.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Dzuwa silidzawamba usana, mwezi sudzakupanda usiku.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Dzuwa silidzakupweteka nthawi ya masana, kapena mwezi nthawi ya usiku.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Dzuwa silidzawamba usana, Mwezi sudzakupanda usiku.