Psalms 121:8 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Chauta adzakusunga kulikonse kumene udzapita, kuyambira tsopano mpaka muyaya.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Yehova adzasungira kutuluka kwako ndi kulowa kwako, kuyambira tsopano kufikira nthawi zonse.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Yehova adzayangʼanira kutuluka kwako ndi kulowa kwako; kuyambira tsopano mpaka muyaya.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Yehova adzasungira kuturuka kwako ndi kulowa kwako, Kuyambira tsopano kufikira nthawi zonse.