Psalms 122:1 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Ndidasangalala pamene adandiwuza kuti, “Tiyeni tipite ku Nyumba ya Chauta.”
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Nyimbo yokwerera; ya Davide. Ndinakondwera m'mene ananena nane, Tiyeni kunyumba ya Yehova.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Salimo la Davide. Nyimbo yoyimba pokwera ku Yerusalemu. Ndinakondwera atandiwuza kuti, “Tiyeni ku nyumba ya Yehova.”
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndinakondwera m'mene ananena nane, Tiyeni ku nyumba ya Yehova.