Psalms 122:4 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Kumeneko kumapita mafuko onse, anthu ake a Chauta, monga momwe adalamulira Israele kuti akayamike dzina la Chauta.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Kumene akwerako mafuko, ndiwo mafuko a Yehova; akhale mboni ya kwa Israele, Ayamike dzina la Yehova.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Kumeneko ndiye kumene kumapita mafuko, mafuko a Yehova, umboni wa kwa Israeli, kuti atamande dzina la Yehova.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Kumene akwerako mafuko, ndiwo mafuko a Yehova; Akhale mboni ya kwa Israyeli, Ayamike dzina la Yehova.