Psalms 122:6 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Pemphererani mtendere wa Yerusalemu ponena kuti, “Anthu amene amakukonda iwe Yerusalemu, zinthu ziziŵayendera bwino.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Mupempherere mtendere wa Yerusalemu; akukonda inu adzaona phindu.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Pemphererani mtendere wa Yerusalemu: “Iwo amene amakukonda iwe zinthu ziwayendere bwino.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Mupempherere mtendere wa Yerusalemu; Akukonda inu adzaona phindu.