Psalms 122:8 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Chifukwa cha abale anga ndi abwenzi anga ndidzanena kuti, “Mtendere ukhaledi m'kati mwako.”
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Chifukwa cha abale anga ndi mabwenzi anga, ndidzanena tsopano, Mukhale mtendere mwa inu.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Chifukwa cha abale anga ndi abwenzi anga ndidzati, “Mtendere ukhale mʼkati mwako.”
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Cifukwa ca abale anga ndi mabwenzi anga, Ndidzanena tsopano, Mukhale mtendere mwa inu.