Psalms 122:9 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Chifukwa cha Nyumba ya Chauta, Mulungu wathu, ndidzakupemphera zabwino.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Chifukwa cha nyumba ya Yehova Mulungu wathu ndidzakufunira zokoma.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Chifukwa cha Nyumba ya Yehova Mulungu wathu, ndidzakufunira zabwino.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Cifukwa ca nyumba ya Yehova Mulungu wathu Ndidzakufunira zokoma,