Psalms 123:1 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Ndikukweza maso anga kwa Inu, Inu amene mumakhala pa mpando wachifumu kumwamba.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Nyimbo yokwerera. Ndikweza maso anga kwa Inu, kwa Inu wakukhala kumwamba.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Nyimbo yoyimba pokwera ku Yerusalemu. Ndikweza maso anga kwa Inu, kwa Inu amene mumakhala kumwamba.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndikweza maso anga kwa Inu, Kwa Inu wakukhala kumwamba.