Psalms 123:4 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Pa nthaŵi yaitali, anthu olemera akhala akutinyodola, anthu onyada akhala akutinyoza.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Moyo wathu wakhuta ndithu ndi kuseka kwa iwo osasowa kanthu, ndi mnyozo wa odzikuza.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Ife tapirira mnyozo wambiri kuchokera kwa anthu odzikuza, chitonzo chachikulu kuchokera kwa anthu onyada.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Moyo wathu wakhuta ndithu Ndi kuseka kwa iwo osasowa kanthu, Ndi mnyozo wa odzikuza.