Psalms 124:7 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Taonjoka ngati mbalame mu msampha wa osaka, msampha wathyoka, ndipo ife tapulumuka.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Moyo wathu unaonjoka ngati mbalame mu msampha wa msodzi; msampha unathyoka ndi ife tinaonjoka.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Moyo wathu wawonjoka ngati mbalame yokodwa mu msampha wa mlenje; msampha wathyoka, ndipo ife tapulumuka.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Moyo wathu unaonjoka ngati mbalame mu msampha wa msodzi; Msampha unatyoka ndi ife tinaonioka.