Psalms 124:8 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Chithandizo chathu chimachokera kwa Chauta, amene adalenga kumwamba ndi dziko lapansi.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Thandizo lathu lili m'dzina la Yehova, wolenga kumwamba ndi dziko lapansi.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Thandizo lathu lili mʼdzina la Yehova wolenga kumwamba ndi dziko lapansi.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Thandizo lathu liri m'dzina la Yehova, Wolenga kumwamba ndi dziko lapansi.