Psalms 125:1 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Anthu amene amakhulupirira Chauta ndi olimba ngati phiri la Ziyoni, limene silingathe kugwedezeka, koma ndi lokhala mpaka muyaya.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Nyimbo yokwerera. Iwo akukhulupirira Yehova akunga phiri la Ziyoni, losasunthika, likhazikika kosatha.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Nyimbo yoyimba pokwera ku Yerusalemu. Amene amadalira Yehova ali ngati phiri la Ziyoni, limene silingagwedezeke koma ndi lokhala mpaka muyaya.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Iwo akukhulupirira Yehova Akunga phiri la Ziyoni, losasunthika, likhazikika kosatha,