Psalms 125:2 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Monga momwe mapiri amazingira Yerusalemu, momwemonso Chauta akuzinga anthu ake kuyambira tsopano mpaka muyaya.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Monga mapiri azinga Yerusalemu, momwemo Yehova azinga anthu ake, kuyambira tsopano kufikira nthawi zonse.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Monga mapiri azungulira Yerusalemu, momwemonso Yehova azungulira anthu ake kuyambira tsopano mpaka muyaya.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Monga mapiri azinga Yerusalemu, Momwemo Yehova azinga anthu ace, Kuyambira tsopano kufikira nthawi zonse.