Psalms 125:4 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Chauta, achitireni zabwino anthu amene ali abwino, amene ali olungama mtima.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Chitirani chokoma, Yehova, iwo okhala okoma; iwo okhala oongoka mumtima mwao.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Yehova chitirani zabwino amene ndi abwino, amene ndi olungama mtima
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Citirani cokoma, Yehova, iwo okhala okoma; Iwo okhala oongoka mumtima mwao.