Psalms 125:5 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Koma anthu amene amatsata njira zao zokhotakhota, Chauta adzaŵapirikitsira kumene kuli anthu ochita zoipa. Mtendere ukhale ndi Israele.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Koma iwo akupatula kutsata njira zao zokhotakhota, Yehova adzawachotsa pamodzi ndi ochita zopanda pake. Mtendere ukhale pa Israele.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Koma amene amatembenukira ku njira zokhotakhota, Yehova adzawachotsa pamodzi ndi anthu ochita zoyipa. Mtendere ukhale pa Israeli.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Koma iwo akupatuka kutsata njira zao zokhotakhota, Yehova adzawacotsa pamodzi ndi ocita zopanda pace. Mtendere ukhale pa Israyeli.