Psalms 126:1 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Pamene Chauta adabwezera akapolo ku Ziyoni, tinali ngati anthu amene akulota.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Nyimbo yokwerera. Pobweza Yehova ukapolo wa Ziyoni, tinakhala ngati anthu akulota.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Nyimbo yoyimba pokwera ku Yerusalemu. Yehova atabwezera akapolo ku Ziyoni, tinali ngati amene akulota.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Pobweza Yehova ukapolo wa Ziyoni, Tinakhala ngati anthu akulota.