Psalms 127:4 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Ana apaunyamata ali ngati mivi m'manja mwa munthu wankhondo.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ana a ubwana wake wa munthu akunga mivi m'dzanja lake la chiphona.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Ana a pa unyamata ali ngati mivi mʼmanja mwa munthu wankhondo.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ana a ubwana wace wa munthu Akunga mibvi m'dzanja lace la ciphona.