Psalms 127:5 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Ngwodala amene phodo lake nlodzaza ndi mivi yotere. Sadzamchititsa manyazi akamalankhula ndi adani ake pa bwalo lamilandu.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Wodala munthu amene anadzaza nayo phodo lake: sadzachita manyazi iwo, pakulankhula nao adani kuchipata.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Wodala munthu amene motengera mivi mwake mwadzaza. Iwo sadzachititsidwa manyazi pamene alimbana ndi adani awo pa zipata.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Wodala munthu amene anadzaza nayo phodo lace: Sadzacita manyazi iwo, Pakulankhula nao adani kucipata.