Psalms 128:2 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Udzadya zimene manja ako adagwirira ntchito. Udzasangalala, ndipo zinthu zidzakuyendera bwino.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Pakuti udzadya za ntchito ya manja ako; wodala iwe, ndipo kudzakukomera.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Udzadya chipatso cha ntchito yako; madalitso ndi chuma zidzakhala zako.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Pakuti udzadya za nchito ya manja ako; Wodala iwe, ndipo kudzakukomera.