Psalms 128:3 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Mkazi wako adzakhala ngati mpesa wobereka, m'kati mwa nyuma yako. Ana ako adzakhala ngati tiziphukira taolivi, kuzungulira tebulo lako.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Mkazi wako adzanga mpesa wopatsa m'mbali za nyumba yako; ana ako adzanga timitengo ta azitona pozinga podyera pako.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Mkazi wako adzakhala ngati mpesa wobereka mʼkati mwa nyumba yako; ana ako adzakhala ngati mphukira za mitengo ya olivi kuzungulira tebulo lako.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Mkazi wako adzanga mpesa wopatsa m'mbali za nyumba yako; Ana ako adzanga timitengo ta azitona pozinga podyera pako.