Psalms 129:1 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
“Adani akhala akundizunza kwambiri kuyambira unyamata wanga,” Israele anene choncho tsopano,
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Nyimbo yokwerera. Anandisautsa kawirikawiri kuyambira ubwana wanga, anene tsono Israele;
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Nyimbo yoyimba pokwera ku Yerusalemu. “Andizunza kwambiri kuyambira ubwana wanga,” anene tsono Israeli;
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Anandisautsa kawiri kawiri kuyambira ubwana wanga, Anene tsono Israyeli;