Psalms 129:2 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
“Adani akhala akundizunza kwambiri kuyambira unyamata wanga, komabe sadandipambane.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Anandisautsa kawirikawiri kuyambira ubwana wanga; koma sanandilake.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
“Andizunza kwambiri kuyambira ubwana wanga, koma sanandipambane.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Anandisautsa kawiri kawiri kuyambira ubwana wanga; Koma sanandilaka.