Psalms 129:4 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Koma Chauta ndi wolungama, wandimasula zingwe za anthu oipa.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Yehova ndiye wolungama; anadulatu zingwe za oipa.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Koma Yehova ndi wolungama; Iye wandimasula ku zingwe za anthu oyipa.”
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Yehova ndiye wolungama; Anadulatu zingwe za oipa.