Psalms 13:2 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Kodi ndizivutika m'maganizo mwanga mpaka liti? Kodi ndiyenera kukhala ndi chisoni mumtima mwanga usana ndi usiku? Kodi mdani wanga azindipambana mpakampaka?
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndidzachita uphungu m'moyo mwanga kufikira liti, pokhala ndi chisoni m'mtima mwanga tsiku lonse? Adzandiukira ine mdani wanga kufikira liti?
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Ndidzalimbana ndi maganizo anga ndi kukhala ndi chisoni mu mtima mwanga tsiku lililonse mpaka liti? Mpaka liti adani anga adzandipambana?
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndidzacita uphungu m'moyo mwanga kufikira liti, Pokhala ndi cisoni m'mtima mwanga tsiku lonse? Adzandiukira ine mdani wanga kufikira liti?