Psalms 13:3 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Mundikumbukire ndipo mundiyankhe, Inu Chauta, Mulungu wanga. Mundiwunikire kuti ndingagone tulo tofa nato.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Penyani, ndiyankheni, Yehova Mulungu wanga. Penyetsani maso anga, kuti ndingagone tulo ta imfa;
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Ndiyangʼaneni ndi kundiyankha, Inu Yehova Mulungu wanga. Walitsani maso anga kuti ndingafe;
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Penyani, ndiyankheni, Yehova Mulungu wanga: Penyetsani maso anga, kuti ndingagone tulo ta imfa;