Psalms 13:5 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Koma ine ndimadalira chikondi chanu chosasinthika. Mtima wanga udzakondwera chifukwa mwandipulumutsa.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Koma ine ndakhulupirira pa chifundo chanu; mtima wanga udzakondwera nacho chipulumutso chanu.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Koma ndikudalira chikondi chanu chosasinthika; mtima wanga umakondwera ndi chipulumutso chanu.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Koma ine ndakhulupira pa cifundo canu; Mtima wanga udzakondwera naco cipulumutso canu: