Psalms 13:6 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Ndidzaimbira Chauta, popeza kuti wandichitira zabwino.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndidzaimbira Yehova, pakuti anandichitira zokoma.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Ine ndidzayimbira Yehova pakuti wandichitira zokoma.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndidzayimbira Yehova, Pakuti anandicitira zokoma.