Psalms 130:2 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Ambuye imvani liwu langa. Tcherani khutu kuti mumve kupemba kwanga.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ambuye, imvani liu langa; makutu anu akhale chimverere mau a kupemba kwanga.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Ambuye imvani mawu anga. Makutu anu akhale tcheru kumva kupempha chifundo kwanga.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ambuye, imvani liu langa; Makutu anu akhale cimverere Mau a kupemba kwanga.