Psalms 130:4 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Koma inu mumakhululukira, nchifukwa chake timakulemekezani.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Koma kwa Inu kuli chikhululukiro, kuti akuopeni.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Koma kwa Inu kuli chikhululukiro; nʼchifukwa chake mumaopedwa.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Koma kwa Inu kuli cikhululukiro, Kuti akuopeni.