Psalms 132:11 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Chauta adalumbirira Davide momtsimikizira, ndipo sadzasintha, adati, “Ndidzakhazika pa mpando wachifumu mmodzi mwa ana ako aamuna.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Yehova analumbira Davide zoona; sadzalibweza; ndi kuti, Wa iwo okhala zipatso za thupi lako ndidzaika pa mpando wachifumu wako.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Yehova analumbira kwa Davide, lumbiro lotsimikizika kuti Iye sadzasintha: “Mmodzi wa ana ako ndidzamuyika pa mpando waufumu;
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Yehova analumbira Davide zoona; Sadzalibweza; ndi kuti, Wa iwo okhala zipatso za thupi lako ndidzaika pa mpando wacifumu wako.