Psalms 132:14 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Akuti, “Ameneŵa ndiwo malo anga opumuliramo mpaka muyaya. Ndidzakhala kuno chifukwa ndakufunitsitsa.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Pampumulo panga mpano posatha, Pano ndidzakhala; pakuti ndakhumbapo.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
“Awa ndi malo anga opumapo ku nthawi za nthawi; ndidzakhala pano pa mpando waufumu, pakuti ndakhumba zimenezi.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Pampumulo panga mpano posatha: Pano ndidzakhala; pakuti ndakhumbapo.