Psalms 132:15 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
“Ndidzadalitsa kwambiri mzinda wa Ziyoni poupatsa zosoŵa zake, anthu ake osauka, ndidzaŵapatsa chakudya chokwanira.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndidzadalitsatu chakudya chake; aumphawi ake ndidzawakhutitsa ndi mkate.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Ndidzadalitsa mzindawu ndi zinthu zambiri; anthu ake osauka ndidzawakhutitsa ndi chakudya.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndidzadalitsatu cakudya cace; Aumphawi ace ndidzawakhutitsa ndi mkate.