Psalms 132:17 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
“Davide ndidzammeretsera chiphukira kumeneko. Ndamkonzera nyale wodzozedwa wanga.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Apo ndidzaphukitsira Davide nyanga; ndakonzeratu wodzozedwa wanga nyali.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
“Pano ndidzachulukitsa mphamvu za Davide ndi kuyikapo nyale ya wodzozedwa wanga.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Apo ndidzaphukitsira Davide nyanga; Ndak onzeraru wodzozedwa wanga nyali.