Psalms 132:18 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Adani ake ndidzaŵaveka manyazi ngati nsalu, koma iye yekhayo adzavala chisoti choŵala chachifumu.”
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndidzawaveka adani ake ndi manyazi; koma pa iyeyu korona wake adzamveka.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Ndidzaveka adani ake manyazi, koma chipewa chaufumu pamutu pake chidzakhala chowala.”
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndidzawabvekaadani ace ndi manyazi Koma pa iyeyu korona wace adzambveka.