Psalms 132:2 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Adalumbira kwa Inu Chauta, nalonjeza kwa Mulungu Wamphamvuzonse wa Yakobe kuti,
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Kuti analumbira Yehova, nawindira Wamphamvuyo wa Yakobo, ndi kuti,
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Iye analumbira kwa Yehova ndi kulonjeza kwa Wamphamvu wa Yakobo kuti,
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Kuti analumbira Yehova, Nawindira Wamphamvuyo wa Yakobo, ndi kuti,