Psalms 132:3 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
“Ndithu sindidzaloŵa m'nyumba mwanga, kapena kukagona pabedi panga,
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ngati ndidzalowa pakhomo pa nyumba yanga, ngati ndidzakwera pa kama logonapo;
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
“Sindidzalowa mʼnyumba mwanga kapena kugona pa bedi langa:
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ngati ndidzalowa pakhomo pa nyumba yanga, Ngati ndidzakwera pa kama logonapo;