Psalms 132:6 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Tidamva za bokosi lachipangano ku Efurata, tidalipeza m'minda ya ku Yaara.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Taonani, tinachimva m'Efurata; tinachipeza kuchidikha cha kunkhalango.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Zoonadi, tinamva za Bokosi la Chipangano ku Efurata, tinalipeza mʼminda ya ku Yaara:
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Taonani, tinacimva m'Efrata; Tinacipeza ku cidikha ca kunkhalango.