Psalms 132:8 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Dzambatukani, Inu Chauta, ndi kupita ku malo anu kumene mumakhala, Inuyo pamodzi ndi bokosi lachipangano lofanizira mphamvu zanu.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ukani, Yehova, lowani ku mpumulo wanu; Inu ndi hema wa mphamvu yanu.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
‘Dzukani Yehova, ndipo bwerani ku malo anu opumulira, Inuyo ndi Bokosi la Chipangano limene limafanizira mphamvu zanu.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ukani, Yehova, lowani ku mpumulo wanu; Inu ndi hema wa mphamvu yanu,