Psalms 132:9 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Ansembe anu avale chilungamo ngati nsalu, anthu anu oyera mtima afuule ndi chimwemwe.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ansembe anu avale chilungamo; ndi okondedwa anu afuule mokondwera.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Ansembe anu avekedwe chilungamo; anthu anu oyera mtima ayimbe nyimbo mwachimwemwe.’ ”
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ansembe anu abvale cilungamo; Ndi okondedwa anu apfuule mokondwera.