Psalms 133:1 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Ati kukoma ndi kukondweretsa ati, anthu akakhala amodzi mwaubale!
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Nyimbo yokwerera; ya Davide. Onani, nkokoma ndi kokondweretsa ndithu kuti abale akhale pamodzi!
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Salimo la Davide. Nyimbo yoyimba pokwera ku Yerusalemu. Onani, nʼkokoma ndi kokondweretsa ndithu pamene abale akhala pamodzi mwachiyanjano!
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Onani, nkokoma ndi kokondweretsa ndithu Kuti abale akhale pamodzi!