Psalms 133:3 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Ndi ngati mame a ku Heremoni, omatsikira ku mapiri a Ziyoni. Ku Ziyoni Chauta amaperekako madalitso, ndiye kuti moyo wamuyaya.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ngati mame a ku Heremoni, akutsikira pa mapiri a Ziyoni. Pakuti pamenepo Yehova analamulira dalitsolo, ndilo moyo womka muyaya.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Zili ngati mame a ku Heremoni otsikira pa Phiri la Ziyoni. Pakuti pamenepo Yehova amaperekapo dalitso, ndiwo moyo wamuyaya.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ngati mame a ku Hermoni, Akutsikira pa mapiri a Ziyoni: Pakuti pamenepo Yehova analamulira dalitsolo, Ndilo moyo womka muyaya,